ZOLINGA ZATHU
Yaulele
Msiku ano anthuakuononga ndalama zochuluka po tsasa malonda chonsecho ma biziness sakuenda, chotelo zikupangisa osasa azipeza ndalama zochuluka kuposa mwini wa bizinesi.mmalo mwake tsamba ili likuika ma biziness anu kwa ulele ngati mwakonda kuziwika paliponse
Yotetezeka komanso yachangu
Chitetezo pa bizinesi chavuta kuika ndiku chosa siku ndi siku katundu pansika zikupangisa biziness kusowa chitetezo kutchingilidwa ndi akuba kapene kuonongeka chifukwa chosanyamula bwino. Pamene mukangoika bizinesi yanu pa samba ili izakhala ikuonedwa ndi aliyense nthawi iliyonse kwina kulikonse
Phindu lathu
Tavitika nthawi yaitali kusasa bizinesi yathu kuzela mmasamba osiyana siyana koma opanda phindu lili lonse ndipano sopano tabwela ndi chiganizo kupanga samba limeneli limene lili lopangidwa mwaukadaulo kusankha zomwe mukufuna mu dela lanu ma bizinesi onse akusonkana pamenepa pamene bizinesi yanu ikuoneka nthawi yomweyo yathunso itha kukhala ndimwai inunso kuiona tonse tikupita chisogolo limozi